Botanix – Buku la zomera

Botanix ya Chicheŵa

NOVODOR FC wolimbana ndi nankafumbwe wa mbatata

Sindikuganiza kuti ndikuyenera kulongosola za nankafumbwe owononga mbewu ya mbatata (Leptinotarsa decemlineata) popeza aliyense akudziwa za chirombo choipachi chimene chimaononga kwambiri mbatata ndipo sikotheka kuzigonjetsa popanda kugwiritsa ntchito mankhwala. Panopa, palibe akudziwa mankhwala enieni amene angagwiritsidwe ntchito pophera nankafumbwe owononga mbewuyu.

Lolemba 12. November 2012 12:21 | purintani | Tizilombo towononga mbewu

Kudzala mababu a maluwa ndi mmera

Chotsani mababu a maluwa ndi mmera amene mwalandira pa positi muphukusi, ndipo zisiyeni zikhale mumthunzi kwa masiku awiri kapena atatu. Chothekera chachiwiri ndikuzidzala nthawi yomweyo ndikuzisunga mumthunzi kwa masiku ochepa kuti zisafote ndi dzuwa.

Loweruka 26. November 2011 14:03 | purintani | Malangizo a kalimidwe ka mbewu

Kulima bowa wa mzikuni (Pleurotus ostreatus)

Bowa wa mzikuni (Pleurotus ostreatus) ndi wotchuka kuposa bowa wamba (champignon mushroom)! tsopano. Kutengera ndi bowa wamba, bowa wa mzikuni uli ndi ubwino umodzi waukulu – sungasokonezedwe ndi chinthu chokupha (Amanita phalloides).

Lachisanu 25. November 2011 15:00 | purintani | Bowa

Pongamia pinnata

chithunzi

Pongamia pinnata

Chinsense Pongamia pinnata (maina ena: Honge Tree, Pongam Tree, Panigrahi) ndi mtengo umene umapululuka masamba nyengo yozizira, pakati pa mamitala 15–25 kutalika, umene uli m’gulu la Fabaceae. Uli ndi m’mwamba mwamukulu ndi maluwa ang’onoang’ono ambiri oyera, pinki kapena violet. Unabadwa ku India, koma unafalikira kulimidwa ku m’mwera chakuvuma kwa Asia.

Lachinayi 24. November 2011 19:59 | purintani | Zomera za chilendo

Kalimidwe ka Four Leaf Clover (Marsilea quadrifolia)

chithunzi

The Four Leaf Clover (Marsilea quadrifolia) ndizomera mmadzi zimene masamba ake amaoneka ngati clover. Mukuganiza kuti pakati pa zomera zammadzi ndi clover palibe ubale? Mbali ina – zonse mwa zinthuzi zikukamba za chikhalidwe cha zomera zosapezekapezeka zokongola kwambiri mu ulimi.

Lachitatu 23. November 2011 19:58 | purintani | Malangizo a kalimidwe ka mbewu

Continue: 1-5 6-10 11-15 16-20 21-22

Mbiri ya KPR

Chizindikiro cha KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera ku Slovakia
KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera la KPR ndi bungwe lapadziko lonse lapansi. Werengani zambiri...
Gawani zomwe mukudziwa za kubyala mbewu komanso kusamalira zomera. Lembani nkhani zokhudza kubzyala ndi kusamalira mbewu komanso zomera, ndi zina zambiri, ndipo zisindikitseni muchinenero chanuchanu mu timabuku tathu ta Botanix! Lumikizanani nafe kuti mumve zambiri.

Category: Zonse Bowa Malangizo a kalimidwe ka mbewu Mapalmu Tizilombo towononga mbewu Udzu Zomera za chilendo Zomera za m’madzi