Botanix – Buku la zomera

Botanix ya Chicheŵa

Kudzala nthanga za mango

Mudzale nthanga za mango zongochotsedwa kumene kuti zimere bwino. Viyikani nthanga m’madzi ndi temperature yokwana 20–25°C kwa pafupifupi maola awiri mpaka asanu ndi imodzi.

Mukanyika, dzalani nthanga m’dothi (dothi la mchenga, lopepuka) ndipo temperature ya mphika isachepere 20–25°C. Nthanga zimamasula ndikuyamba kumera mkati mwa mulungu umodzi mpaka milungu itatu. Zomera zongoyamba kumene zisungidwe podutsa dzuwa locheperako.

Ngati mukukhala ku madera otentha, mukhonza kudzala mbewu ya mango mudimba/mmunda mwanu. Ngati mumakhala kumadera ozizira kapena kumene madzi amafika poundana chifukwa chakuzizira kwambiri, ndibwino kusunga mbewu ya mango mkati mwa nyumba kapena m’nyumba ya zomera.

««« Nkhani ya m’mbuyo: Mango a Kalimantan, Kasturi (Mangifera casturi) Nkhani yotsatira: Kalimidwe ka Four Leaf Clover (Marsilea quadrifolia) »»»

Lachiwiri 22. November 2011 19:57 | purintani | Zomera za chilendo, Malangizo a kalimidwe ka mbewu

Mbiri ya KPR

Chizindikiro cha KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera ku Slovakia
KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera la KPR ndi bungwe lapadziko lonse lapansi. Werengani zambiri...
Gawani zomwe mukudziwa za kubyala mbewu komanso kusamalira zomera. Lembani nkhani zokhudza kubzyala ndi kusamalira mbewu komanso zomera, ndi zina zambiri, ndipo zisindikitseni muchinenero chanuchanu mu timabuku tathu ta Botanix! Lumikizanani nafe kuti mumve zambiri.

Category: Zonse Bowa Malangizo a kalimidwe ka mbewu Mapalmu Tizilombo towononga mbewu Udzu Zomera za chilendo Zomera za m’madzi